1 Chronicles 3:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Hananiya naŵa: Pelatiya, Yesaya, Refaya, Arinani, Obadiya ndi Sekaniya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana a Hananiya: Pelatiya, ndi Yesaya, ana a Refaya, ana a Arinani, ana a Obadiya, ana a Sekaniya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zidzukulu za Hananiya zinali izi: Pelatiya ndi Yesaiya, ndiponso ana a Refaya, ana a Arinani, ana a Obadiya ndi ana a Sekaniya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana a Hananiya: Pelatiya, ndi Yesaya, ana a Refaya, ana a Arinani, ana a Obadiya, ana a Sekaniya.