1 Chronicles 3:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wa Sekaniya anali Semaya. Ana a Semaya naŵa: Hatusi, Igala, Bariya, Neariya ndi Safati, asanu ndi mmodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi mwana wa Sekaniya: Semaya; ndi ana a Semaya: Hatusi, ndi Igala, ndi Bariya, ndi Neariya, ndi Safati; asanu ndi mmodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zidzukulu za Sekaniya zinali izi: Semaya ndi ana ake: Hatusi, Igala, Bariya, Neariya ndi Safati. Onse anali asanu ndi mmodzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi mwana wa Sekaniya: Semaya; ndi ana a Semaya: Hatusi, ndi Igali, ndi Bariya, ndi Neariya, ndi Safati; asanu ndi mmodzi.