1 Chronicles 3:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Neariya, naŵa: Eliyoenai, Hizikiya ndi Azirikamu, atatu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana a Neariya: Eliyoenai, ndi Hizikiya, ndi Azirikamu, atatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Neariya anali awa: Eliyoenai, Hezekiya ndi Azirikamu. Onse anali atatu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana a Neariya: Eliunai, ndi Hizikiya, ndi Azrikamu, atatu.