1 Chronicles 3:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Eliyoenai, naŵa: Hodaviya, Eliyasibu, Pelaya, Akubu, Yohanani, Delaya ndi Anani, asanu ndi aŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana a Eliyoenai: Hodaviya, ndi Eliyasibu, ndi Pelaya, ndi Akubu, ndi Yohanani, ndi Delaya, ndi Anani, asanu ndi awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Eliyoenai: Hodaviya, Eliyasibu, Pelaya, Akubu, Yohanani, Delaya ndi Anani, onse anali asanu ndi awiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana a Eliunai: Hodavia, ndi Eliasibu, ndi Pelaya, ndi Akubu, ndi Yohanana, ndi Delaya, ndi Anani, asanu ndi awiri.