1 Chronicles 3:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana amene adabadwira ku Yerusalemu ndi aŵa: Simea, Sobabu, Natani ndi Solomoni. Ameneŵa ndiwo ana anai amene adamubalira Batisuwa mwana wa Amiyele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ombadwira m'Yerusalemu ndi awa: Simea, ndi Sobabu, ndi Natani, ndi Solomoni, anai a Batisuwa mwana wamkazi wa Amiyele;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo ana amene anabadwira ku Yerusalemuko anali awa: Samua, Sobabu, Natani ndi Solomoni. Ana anayi awa anali a Batisuwa mwana wa Amieli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ombadwira m'Yerusalemu ndi awa: Simeya, ndi Sobabu, ndi Natani, ndi Solomo, anai a Batisuwa mwana wamkazi wa Amieli;