1 Chronicles 4:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Esitoni adabereka Beterafa, Paseya ndi Tehina, tate wa Irinahasi. Ameneŵa ndiwo anthu a ku Reka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Esitoni, anabala Beterafa, ndi Paseya, ndi Tehina atate wa Irinahasi. Awa ndi anthu a Reka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Esitoni anabereka Beti-Rafa, Paseya ndi Tehina amene anabereka Iri Nahasi. Amenewa ndiwo anthu a ku Reka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi Esitoni anabala Betirafa, ndi Paseya, ndi Tehina atate wa Irinahasi. Awa ndi anthu a Reka.