1 Chronicles 4:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Kenazi naŵa: Otiniyele ndi Seraya. Ana a Otiniyele naŵa: Hatati ndi Meonotai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana a Kenazi: Otiniyele, ndi Seraya; ndi mwana wa Otiniyele: Hatati.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Kenazi anali awa: Otanieli ndi Seraya. Ana a Otanieli anali awa: Hatati ndi Meonotai.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana a Kenazi: Otiniyeli, ndi Seraya; ndi mwana wa Otmiyeh: Hatati.