1 Chronicles 4:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Meonotai adabereka Ofura. Ndipo Seraya adabereka Yowabu, tate wa Ageharasimu. Adaŵatcha choncho popeza kuti anali anthu azaluso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Meonotai anabala Ofura; ndi Seraya anabala Yowabu atate wa Geharasimu; popeza iwo ndiwo amisiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Meonotai anabereka Ofura. Seraya anabereka Yowabu, amene anabereka Ge-Harasimu. Anawatcha dzina ili chifukwa anthu ake anali amisiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Meonotai anabala Ofra; ndi Seraya anabala Yoabu atate wa Geharasimu; popeza iwo ndiwo amisiri.