1 Chronicles 4:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Kalebe, mwana wa Yefune, naŵa: Iru, Ela, ndi Naamu. Mwana wa Ela anali Kenazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana a Kalebe mwana wa Yefune: Iru, Ela, ndi Naamu; ndi ana a Ela, ndi Kenazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Kalebe mwana wa Yefune anali awa: Iru, Ela ndi Naama. Mwana wa Ela anali Kenazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana a Kalebi mwana wa Yefune: Iru, Ela, ndi Naamu; ndi ana a Ela, ndi Kenazi.