1 Chronicles 4:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a mkazi wa Hodiya, mlongo wake wa Nahamu, ndiwo adabereka Keila Mgarimi ndiponso Esitemowa Mmaakati.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana a mkazi wa Hodiya, mlongo wake wa Nahamu, ndiwo atate a Keila Mgarimi ndi Esitemowa Mmaaka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a mkazi wa Hodiya, mlongo wa Nahamu anali awa: abambo ake a Keila wa ku Garimi ndi Esitemowa wa ku Maaka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana a mkazi wa Hodiya, mlongo wace wa Nahamu, ndiwo atate a Kula Mgarimi ndi Esitemowa Mmaaka.