1 Chronicles 4:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ameneŵa anali anthu oumba mbiya ndiponso nzika za ku Netaimu ndi ku Gedera. Adakhala kumeneko pamodzi ndi mfumu, namaigwirira ntchito.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo ndiwo oumba mbiya, ndi okhala m'Netaimu, ndi m'Gedera; anakhala komweko ndi mfumu m'ntchito yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anali owumba mbiya amene ankakhala ku Netaimu ndi Gederi. Ankakhala kumeneko ndi kumatumikira mfumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo ndiwo oumba mbiya, ndi okhala m'Netaimu, ndi m'Gedera; anakhala komweko ndi mfumu m'nchito yace.