1 Chronicles 4:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Misima naŵa: Hamuele kudzanso Zakuli ndi Simei.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana a Misima: Hamuele mwana wake, Zakuri mwana wake, Simei mwana wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zidzukulu za Misima zinali izi: Hamueli, Zakuri ndi Simei.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana a Misma: Hamueli mwana wace, Zakuri mwana wace, Simei mwana wace.