1 Chronicles 4:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Betemara-Kaboti, Hazara-Susimu, Betebiri ndiponso ku Saaraimu. Imeneyi inali mizinda yao mpaka nthaŵi imene Davide adayamba kulamulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi ku Betemara-Kaboti, ndi ku Hazara-Susimu, ndi ku Betebiri, ndi ku Saaraimu. Iyi ndi midzi yao, mpaka ufumu wa Davide, pamodzi ndi milaga yao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Beti-Marikaboti, Hazari-Susimu, Beti-Biri ndi Saaraimu. Iyi inali mizinda yawo mpaka pa nthawi ya ulamuliro wa Davide.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi ku Betimarikaboti, ndi ku Hazarasusimu, ndi ku Betibiri, ndi ku Saraimu. Iyi ndi midzi yao, mpaka ufumu wa Davide, pamodzi ndi miraga yao.