1 Chronicles 4:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pamodzi ndi midzi yao ina yozungulira mizinda imeneyi, mpaka kukafika ku Baala. Kumeneku ndiko kumene ankakhala ndipo ankasunga mndandanda wa maina.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi milaga yao yonse pozungulira pake pa midzi yomweyi, mpaka Baala. Apo ndi pokhala pao ndipo ali nao mawerengedwe a maina ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndi midzi yonse yozungulira mizinda imeneyi mpaka ku Baala. Awa anali malo awo okhalapo. Ndipo anasunga mbiri ya makolo awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi miraga yao yonse pozungulira pace pa midzi yomweyi, mpaka Baala. Apo ndi pokhala pao ndipo ali nao mawerengedwe a maina ao.