1 Chronicles 4:38 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu amene tatchulaŵa ndiwo anali atsogoleri a mabanja ao, ndipo mabanja a makolo ao adaonjezeka kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
awa otchedwa maina ndiwo akalonga m'mabanja ao, ndi nyumba za makolo ao zinachuluka kwambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu amene atchulidwawa anali atsogoleri a mabanja awo. Mabanja awo anakula kwambiri
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
awa ochedwa maina ndiwo akalonga m'mabanja ao, ndi nyumba za makolo ao zinacuruka kwambiri.