1 Chronicles 4:39 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero adapita cha kunja kwa mudzi wa Gedori, kuvuma kwa chigwa, kuti akafunefune busa la ziweto zao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anamuka mpaka polowera ku Gedori kum'mawa kwa chigwa, kufunafuna podyetsa zoweta zao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo anakafika ku malire a Gedori ku chigwa cha kummawa kufuna msipu wodyetsa ziweto zawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anamuka mpaka polowera ku Gedoro kum'mawa kwa cigwa, kufunafuna podyetsa zoweta zao.