1 Chronicles 4:40 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumeneko adakapezako busa lokoma ndi la msipu wambiri. Dziko lakenso linali lalikulu, labata ndi laufulu. Anthu amene ankakhala kumeneko kale anali Ahamu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapeza podyetsa ponenepetsa ndi pabwino, ndipo dzikoli ndi lachitando ndi lodikha ndi losungikamo, pakuti okhalako kale ndiwo a Hamu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anapeza msipu wobiriwira ndi wabwino ndipo dziko linali lalikulu, la mtendere ndi bata. Kumeneko kunkakhala fuko la Hamu poyamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapeza podyetsa ponenepetsa ndi pabwino, ndipo dzikoli ndi lacitando ndi lndikha ndi losungikamo, pakuti okhalako kale ndiwo a Hamu.