1 Chronicles 4:42 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Asimeoni ena okwanira mazana asanu, adapita ku phiri la Seiri. Atsogoleri ao anali Pelatiya, Neyariya, Refaya ndi Uziyele, ana a Isi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ena a iwowa a ana a Simeoni, amuna mazana asanu, ananka kuphiri la Seiri; akuwatsogolera ndiwo Pelatiya, ndi Neariya, ndi Refaya, ndi Uziyele; ana a Isi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anthu 500 a fuko la Simeoni, motsogozedwa ndi Pelatiya, Neariya, Refaya ndi Uzieli, ana a Isi, analanda dziko lamapiri la Seiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ena a iwowa a ana a Simeoni, amuna mazana asanu, anamka ku phiri la Seiri; akuwatsogolera ndiwo Pelatiya, ndi Neariya, ndi Refaya, ndi Uzieli; ana a lsi.