1 Chronicles 4:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kozi adabereka Anubu, Zobeba, ndi mabanja a Ahariyele, mwana wa Harumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Hakozi anabala Anubu, ndi Zobeba, ndi mabanja a Ahariyele mwana wa Harumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndi Kozi, amene anali abambo ake a Anubi ndi Hazo-Beba ndi mabanja a Ahariheli mwana wa Harumi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Hakozi anabala Anubu, ndi Zobeba, ndi mabanja a Ahareli mwana wa Harumu.