1 Chronicles 5:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa nthaŵi ya Saulo, Arubeni adathira nkhondo Ahagiri ndi kuŵagonjetsa, kenaka adakhala m'mahema mwao m'dziko lonselo kuvuma kwa Giliyadi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo masiku a Saulo anagwirana nkhondo ndi Ahagiri, amene adagwa ndi dzanja lao; ndipo anakhala m'mahema mwao kum'mawa konse kwa Giliyadi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa nthawi ya Sauli anachita nkhondo ndi Ahagiri ndi kuwagonjetsa. Tsono iwo anakhala mʼmatenti a Ahagiri ku dera lonse la kummawa kwa Giliyadi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo masiku a Sauli anagwirana nkhondo ndi Ahagiri, amene adagwa ndi dzanja lao; ndipo anakhala m'mahema mwao kum'mawa konse kwa Gileadi.