1 Chronicles 5:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Gadi adakhala kumpoto kwa Arubeni m'dziko la Basani mpaka kukafika ndithu kuvuma ku Saleka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana a Gadi anakhala pandunji pao m'dziko la Basani mpaka Saleka:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu a fuko la Gadi anakhala moyandikana ndi fuko la Rubeni ku Basani mpaka ku Saleka:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana a Gadi anakhala pandunji pao m'dziko la Basana mpaka Saleka: