1 Chronicles 5:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ahi, mwana wa Abidiyele, mwana wa Guni, ndiye amene anali mfumu ya mabanja a makolo ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ahi mwana wa Abidiyele, mwana wa Guni, ndiye mkulu wa nyumba za makolo ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ahi mwana wa Abdieli, mwana wa Guni, anali mtsogoleri wa banja la makolo awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ahi mwana wa Abdieli, mwana wa Guni, ndiye mkulu wa nyumba za makolo ao.