1 Chronicles 5:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma a fuko la Yuda anali amphamvu pakati pa mafuko a Israele, ndipo mfumu idachokera kwa iwowo, ngakhale kuti ukulu wa uchisamba unali wa Yosefe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Yuda anakula mphamvu mwa abale ake, ndi mtsogoleri anafuma kwa iyeyu, koma ukulu ngwa Yosefe);
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo ngakhalenso Yuda anali wamphamvu kwambiri pakati pa abale ake, ndi kuti wolamulira anachokera mwa iye, ulemu wa mwana woyamba kubadwa unaperekedwa kwa Yosefe)
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Yuda anakula mphamvu mwa abale ace, ndi mtsogoleri anafuma kwa iyeyu, koma ukulu ngwa Yosefe);