1 Chronicles 5:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaŵalanda ziŵeto zao monga izi: ngamira zokwanira 50,000, nkhosa zokwanira 250,000, abulu okwanira 2,000. Adagwiranso anthu amoyo okwanira 100,000.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo analanda zoweta zao, ngamira zao zikwi makumi asanu, ndi nkhosa zikwi mazana awiri ndi makumi asanu, ndi abulu zikwi ziwiri, ndi amuna zikwi zana limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho iwo analanda ziweto za Ahagiri: ngamira 50,000, nkhosa ndi mbuzi 250,000 ndi abulu 2,000. Ndiponso anagwira akapolo 100,000,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo analanda zoweta zao, ngamila zao zikwi makumi asanu, ndi nkhosa zikwi mazana awiri ndi makumi asanu, ndi aburu zikwi ziwiri, ndi amuna zikwi zana limodzi.