1 Chronicles 5:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Theka la fuko la Manase linkakhala m'dziko lakuvuma kuyambira ku Basani mpaka ku Baala-Heremoni, Seniri ndiponso ku phiri la Heremoni. Anthuwo anali ochuluka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana a limodzi la magawo awiri a fuko la Manase anakhala m'dziko; anachuluka kuyambira Basani kufikira Baala-Heremoni, ndi Seniri, ndi phiri la Heremoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Theka la fuko la Manase linkakhala ku dziko la kummawa kuyambira ku Basani mpaka ku Baala-Herimoni, kumene ndi ku Seniri (Phiri la Herimoni) ndipo anthuwo anali ochuluka kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana a limodzi la magawo awiri a pfuko la Manase anakhala m'dziko; anacuruka kuyambira Basana kufikira Baala Herimoni, ndi Seniri, ndi phiri la Herimoni.