1 Chronicles 5:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ana a Rubeni naŵa: Hanoki, Palu, Hezironi ndi Karimi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ana a Rubeni mwana woyamba wa Israele: Hanoki, ndi Palu, Hezironi, ndi Karimi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ana a Rubeni mwana woyamba wa Israeli ndi awa: Hanoki, Palu, Hezironi, ndi Karimi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ana a Rubeni mwana woyamba wa Israyeli: Hanoki, ndi Palu, Hezroni, ndi Karmi.