1 Chronicles 5:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akuluakulu a fuko la Rubeni, potsata mndandanda wa maina ao, naŵa: mtsogoleri Yeiyele, Zekariya,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi abale ake monga mwa mabanja ao, powerenga chibadwidwe cha mibadwo yao: akulu ndiwo Yeiyele, ndi Zekariya,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abale awo mwa mabanja awo, potsata mndandanda wa mʼbado wawo, ndi awa: Yeiyeli, mtsogoleri, Zekariya,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi abale ace monga mwa mabanja ao, powerenga cibadwidwe ca mibadwo yao: akuru ndiwo Yeyeli, ndi Zekariya,