1 Chronicles 5:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndiponso Bela mwana wa Azazi, mwana wa Sema, wa banja la Yowele. Onsewo ankakhala ku Aroere mpaka kukafika ku Nebo ndi ku Baala-Meoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Bela mwana wa Azazi, mwana wa Sema, mwana wa Yowele, wokhala ku Aroere, ndi kufikira ku Nebo ndi Baala-Meoni;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndiponso Bela mwana wa Azazi, mwana wa Sema, mwana wa Yoweli. Iwo ankakhala ku Aroeri mpaka ku Nebo ndi Baala-Meoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Bela mwana wa Azazi, mwana wa Sema, mwana wa Yoeli, wokhala ku Aroeri, ndi kufikira ku Nebo ndi Baala-meoni;