1 Chronicles 5:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwowo adakhala kuvuma mpaka kukafika poloŵera m'chipululu cha mbali ina ya Yufurate, chifukwa chakuti ng'ombe zao zinali zitaswana kwambiri m'dziko la Giliyadi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kum'mawa anakhala mpaka polowera kuchipululu kuyambira mtsinje wa Yufurate; pakuti zoweta zao zinachuluka m'dziko la Giliyadi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anakhala cha kummawa mpaka kukafika polowera mʼchipululu cha mbali ina ya Mtsinje wa Yufurate, chifukwa ziweto zawo zinaswana kwambiri mʼdziko la Giliyadi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kum'mawa anakhala mpaka polowera kucipululu kuyambira mtsinje wa Firate; pakuti zoweta zao zinacuruka m'dziko la Gileadi.