1 Chronicles 6:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yohanani adabereka Azariya (ndi iyeyu uja ankatumikira za unsembe ku nyumba imene Solomoni adamanga ku Yerusalemu).
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Yohanani anabala Azariya (ndiye amene anachita ntchito ya nsembe m'nyumba anaimanga Solomoni m'Yerusalemu),
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yohanani anabereka Azariya (uyu ndi amene anatumikira monga wansembe mʼNyumba ya Mulungu imene Solomoni anamanga mu Yerusalemu),
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Yohanani anabala Azariya (ndiye amene anacita nchito ya nsembe m'nyumba anaimanga Solomo m'Yerusalemu),