1 Chronicles 6:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Samuele naŵa: Yowele mwana wake wachisamba, Abiya mwana wake wachiŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana a Samuele: woyamba Yowele, ndi wachiwiri Abiya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Samueli ndi awa: Mwana wake woyamba anali Yoweli, wachiwiri anali Abiya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana a Samueli: woyamba Yoeli, ndi waciwiri Abiya.