1 Chronicles 6:39 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Panalinso mbale wake Asafu amene ankatsogolera gulu lachiŵiri la oyimba. Asafuyo anali mwana wa Berekiya, mwana wa Simea.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi mbale wake Asafu wokhala ku dzanja lake lamanja, ndiye Asafu mwana wa Berekiya, mwana wa Simea,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndi Asafu mʼbale wake, amene ankatumikira ku dzanja lake lamanja: Asafu anali mwana wa Berekiya, mwana wa Simea,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi mbale wace Asafu wokhala ku dzanja lace lamanja, ndiye Asafu mwana wa Berekiya, mwana wa Simeya,