1 Chronicles 6:48 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo abale ao Alevi ndiwo amene adasankhidwa kuti azigwira ntchito zonse za m'chihema cha Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi abale ao Alevi anaikidwa achite za utumiki zilizonse za Kachisi wa nyumba ya Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abale awo Alevi anapatsidwa ntchito zina zonse ku malo opatulika ku nyumba ya Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi abale ao Alevi anaikidwa acite za utumiki ziti zonse za kacisi wa nyumba ya Mulungu.