1 Chronicles 6:54 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Naŵa malo ao kumene ankakhala potsata malire a malowo: Zidzukulu za Aroni za m'mabanja a Kohati zidalandira chigawo choyamba,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pokhala pao tsono monga mwa madera ao m'malire mwao ndi awa: kwa ana a Aroni a mabanja a Akohati, pakuti maere oyamba adagwera iwowa,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Malo amene iwo anapatsidwa kuti likhale dziko lawo ndi awa: (Malowa anapatsidwa kwa zidzukulu za Aaroni zimene zinali za banja la Kohati, chifukwa malo oyamba kugawidwa anali awo).
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pokhala pao tsono monga mwa madera ao m'malire mwao ndi awa: kwa ana a Aroni a mabanja a Akobati, pakuti maere oyamba adagwera iwowa,