1 Chronicles 6:55 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndiye kuti Hebroni, m'dziko la Yuda pamodzi ndi mabusa omwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kwa iwo anapereka Hebroni m'dziko la Yuda, ndi podyetsa pake pozungulira pake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anapatsidwa Hebroni mʼdziko la Yuda ndi madera odyetsera ziweto ozungulira malowa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kwa iwo anapereka Hebroni m'dziko la Yuda, ndi podyetsa pace pozungulira pace;