1 Chronicles 6:56 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma minda ndi miraga ya mzindawo adaipatsa Kalebe mwana wa Yefune.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma minda ya mudzi ndi milaga yake anapatsa Kalebe mwana wa Yefune.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma minda ndi midzi yozungulira mzindawo zinapatsidwa kwa Kalebe mwana wa Yefune.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma minda ya mudzi ndi miraga yace anapatsa Kalebi mwana wa Yefune.