1 Chronicles 6:61 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adachita maele ndipo Akohati otsala adaŵagawira midzi khumi kuchokera pa fuko lahafu la Manase.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo otsala a ana a Kohati analandira mwa maere, motapa pa mabanja a fuko, pa fuko la Manase logawika pakati, midzi khumi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zidzukulu zotsala za Kohati anazigawira midzi khumi kuchokera ku mabanja a fuko la theka la Manase.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo otsala a ana a Kohati analandira mwa maere, motapa pa mabanja a pfuko, pa pfuko la Manase logawika pakati, midzi khumi.