1 Chronicles 6:62 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ageresomo, potsata mabanja ao, adaŵagawira mizinda khumi ndi itatu kuchokera pa mafuko a Isakara, Asere, Nafutali ndiponso Manase ku Basani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi kwa ana a Geresomo monga mwa mabanja ao, motapa pa fuko la Isakara, ndi pa fuko la Asere, ndi pa fuko la Nafutali, ndi pa fuko la Manase m'Basani, midzi khumi ndi itatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zidzukulu za Geresomu banja ndi banja zinapatsidwa mizinda 13 kuchokera ku mafuko a Isakara, Aseri ndi Nafutali, ndi gawo lina la fuko la Manase limene lili ku Basani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi kwa ana a Gerisomu monga mwa mabanja ao, motapa pa pfuko la Isakara, ndi pa pfuko la Aseri, ndi pa pfuko la Nafitali, ndi pa pfuko la Manase m'Basana, midzi khumi ndi itatu.