1 Chronicles 6:63 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amerari, potsata mabanja ao, adaŵagawira mizinda khumi ndi iŵiri kuchokera pa mafuko a Rubeni, Gadi ndi Zebuloni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Merari analandira mwa maere monga mwa mabanja ao, motapa pa fuko la Rubeni, ndi pa fuko la Gadi, ndi pa fuko la Zebuloni, midzi khumi ndi iwiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zidzukulu za Merari banja ndi banja zinapatsidwa mizinda khumi ndi iwiri kuchokera ku mafuko a Rubeni, Gadi ndi Zebuloni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Merari analandira mwa maere monga mwa mabanja ao, motapa pa pfuko la Rubeni, ndi pa pfuko la Gadi, ndi pa pfuko la Zebuluni, midzi khumi ndi iwiri.