1 Chronicles 6:65 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atachita maele, adaŵapatsanso mizinda ija imene inali ya mafuko a Yuda, Simeoni ndi Benjamini.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapatsa mwamaere, motapa pa fuko la ana a Yuda, ndi pa fuko la Simeoni, ndi pa fuko la ana a Benjamini, midzi iyi yotchulidwa maina ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuchokera ku mafuko a Yuda, Simeoni ndi Benjamini anawapatsa mizinda imene inawatchula kale mayina.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapatsa mwamaere, motapa pa pfuko la ana a Yuda, ndi pa pfuko la Simeoni, ndi pa pfuko la ana a Benjamini, midzi iyi yochulidwa maina ao.