1 Chronicles 7:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Isakara naŵa: Tola, Puwa, Yasubu, ndi Simironi, anai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Isakara ndiwo Tola, ndi Puwa, Yasubu ndi Simironi; anai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Isakara anali awa: Tola, Puwa, Yasubu ndi Simironi ndipo onse analipo anayi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Isakara ndiwo Tola, ndi Pua, Yasubu ndi Simironi; anai.