1 Chronicles 7:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Supimu ndi Hupimu anali ana a Iri, ndipo analinso a fuko ili. Husimu anali mwana wa Dan.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Supimu yemwe ndi Hupimu ana a Iri, ndi Husimu mwana wa Aheri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Asupi ndi Ahupi anali zidzukulu za Iri, ndipo Ahusimu anali zidzukulu za Aheri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sufimu yemwe ndi Hupimu ana a Iri, ndi Husimu mwana wa Aheri.