1 Chronicles 7:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Manase naŵa: Asiriele amene adamuberekera mzikazi wake wa ku Aramu. Mkazi yemweyo adabalanso Makiri, bambo wake wa Giliyadi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Manase ndiwo Asiriele amene mkazi wake anambala. Koma mkazi wake wamng'ono Mwaramu anabala Makiri atate wa Giliyadi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Manase anali awa: Asirieli ndi mwana amene anabereka kwa mzikazi wake wa ku Aramu. Mzikazi yemweyo anaberekanso Makiri abambo ake a Giliyadi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Manase ndiwo Asrieli amene mkazi wace anambala, Koma mkazi wace wamng'ono Maramu anabala Makiri atate wa Gileadi;