1 Chronicles 7:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Maaka, mkazi wa Makiri, adabala mwana wamwamuna, namutcha dzina loti Peresi. Mbale wake anali Seresi, ndipo ana ake aamuna anali Ulamu ndi Rakemu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Maaka mkazi wa Makiri anabala mwana, namutcha dzina lake Peresi, ndi dzina la mbale wake ndiye Seresi, ndi ana ake ndiwo Ulamu, ndi Rakemu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Maaka mkazi wa Makiri anabereka mwana wamwamuna ndipo anamutcha Perezi. Mʼbale wake anamutcha Seresi, ndipo ana ake anali Ulamu ndi Rakemu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi Maaka mkazi wa Makiri anabala mwana, namucha dzina lace Peresi, ndi dzina la mbale wace ndiye Seresi, ndi ana ace ndiwo Ulamu, ndi Rakemu.