1 Chronicles 7:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wa Ulamu anali Bedani. Ameneŵa anali ana a Giliyadi, mwana wa Makiri, mwana wa Manase.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi mwana wa Ulamu: Bedani; ndiwo ana a Giliyadi mwana wa Makiri mwana wa Manase.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wa Ulamu anali Bedani. Awa anali ana a Giliyadi mwana wa Makiri, mwana wa Manase.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi mwana wa Ulamu: Bedani; ndiwo ana a Gileadi mwana wa Makiri mwana wa Manase.