1 Chronicles 7:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zabadi, Sutela. Efuremu anali nawonso ana aŵiri: Ezere ndi Eleadi amene adaphedwa ndi anthu a ku Gati eni ake a dzikolo, chifukwa chakuti adabwera kudzalanda ng'ombe zao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Zabadi mwana wake, ndi Sutela mwana wake, ndi Ezere, ndi Eleadi, amene anthu a Gati obadwa m'dziko anamupha, popeza anatsikira kukalanda zoweta zao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zabadi, Sutela. Ezeri ndi Eladi anaphedwa ndi anthu a ku Gati, pamene anabwera kudzalanda zoweta zawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Zabadi mwana wace, ndi Sutela mwana wace, ndi Ezeri, ndi Eleadi, amene anthu a Gadi obadwa m'dziko anamupha, popeza anatsikira kukalanda zoweta zao.