1 Chronicles 7:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wake wamkazi anali Seera, amene adamanga mzinda wa Betehoroni wakunsi ndi Betehoroni wakumtunda, kudzanso Uzeniseera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mwana wake wamkazi ndiye Seera, amene anamanga Betehoroni wa kunsi, ndi Betehoroni wa kumtunda, ndi Uzeniseera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wake wamkazi anali Seera, amene anamanga mzinda wa Beti-Horoni Wakumunsi, Wakumtunda kudzanso Uzeni-Seera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mwana wace wamkazi ndiye Seera, amene anamanga Beti-horoni wa kunsi, ndi Beti-horoni wa kumtunda, ndi Uzeniseera.