1 Chronicles 7:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wina wa Efuremu anali Refa, amene zidzukulu zake zinali izi: Resefi, Tela, Tahani,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Refa anali mwana wake, ndi Resefi, ndi Tela mwana wake, ndi Tahani mwana wake,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wina wa Efereimu anali Refa amene zidzukulu zake zinali Resefu, Tela, Tahani,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Refa anali mwana wace, ndi Resefe, ndi Tela mwana wace, ndi Tahani mwana wace,