1 Chronicles 7:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maiko ao kumene ankakhala anali Betele pamodzi ndi midzi yake. Chakuvuma kunali Naarani, chakuzambwe kunali Gezere pamodzi ndi midzi yake, Sekemu pamodzi ndi midzi yake, ndiponso Aya pamodzi ndi midzi yake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo dziko lao, ndi pokhala pao ndizo Betele ndi milaga yake, ndi kum'mawa Naarani, ndi kumadzulo Gezere ndi milaga yake, ndi Sekemu ndi milaga yake, mpaka Aya ndi milaga yake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Malo amene ankakhala anali Beteli ndi midzi yozungulira, cha kummawa kunali Naarani, Gezeri ndi midzi yake ya kumadzulo ndi Sekemu ndi midzi yake mpaka ku Aya ndi midzi yake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo dziko lao, ndi pokhala pao ndizo Beteli ndi miraga yace, ndi kum'mawa Narani, ndi kumadzulo Gezeri ndi miraga yace, ndi Sekemu ndi miraga yace, mpaka Aza ndi miraga yace;