1 Chronicles 7:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamodzi ndi iwowo, malinga ndi mibadwo yao ndi mabanja a makolo ao, panali anthu ankhondo 36,000, pakuti anali ndi akazi ambiri ndiponso ana ambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi pamodzi nao mwa mibadwo yao, mwa nyumba za makolo ao, panali magulu a nkhondo zikwi makumi atatu mphambu zisanu ndi chimodzi, popeza anachuluka akazi ao ndi ana ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga mwa chiwerengero cha mabanja awo, panali anthu 36,000 odziwa kumenya nkhondo, pakuti iwo anali ndi akazi ndi ana ambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi pamodzi nao mwa mibadwo yao, mwa nyumba za makolo ao, panali magulu a nkhondo zikwi makumi atatu mphambu zisanu ndi cimodzi, popeza anacuruka akazi ao ndi ana ao.